Kwanu Ndi kwanu by Jeg Tellem Lyrics
Looking for the Chichewa lyrics to “Kwanu Ndi kwanu” by Jeg Tellem (2022)? More than 169 people have already found the lyrics of the song for karaoke, the notes of the melody to the song, the official video and clip of the song “Kwanu Ndi kwanu”.
Quote from the song “Kwanu Ndi kwanu” by Jeg Tellem
Woyee yeah yeah
Osamayiwala kwanu
Tellem
Osamayiwala
LyricsWord.com
Can you finish lyrics of the song “Kwanu Ndi kwanu” based on this quote?
If you can't then the lyrics will be below ...
Credits, Cast & Crew of Song “Kwanu Ndi kwanu”
- Featuring: 6th Mw, K Banton, LJ Woyee, Earnestar
- Produced: Nic Nather
- Written: Joy Gondwe
- Release Date:
Additional Information About the Sample “Kwanu Ndi kwanu”:
- Featuring: 6th Mw, K Banton, LJ Woyee, Earnestar rn
- Produced: Nic Nather rn
- Written: Joy Gondwe
Perfect Lyrics of the Song “Kwanu Ndi kwanu” Released in 2022
[Favorite Song Lyrics: song “Kwanu Ndi kwanu” with perfect lyrics for karaoke]
Woyee yeah yeah
Osamayiwala kwanu
Tellem
Osamayiwala
Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mhuuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mhhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Nthengo mudalaka njoka aaah
Penapake zikavuta iwe
Ndikwanube
Usamachite manyazi
Ndikwanube
Utha kubwerera konko
Ndikwanube ah ah aaaaah
Osayi wala
Dzuwa likawala
Yemwe anakubala
Yemwe anakusamala
Pamene ukudwala
Usanakwela ladder
Kwanu kwanu nthengo mudalaka njoka
Uzakufunabe olo utachoka
Mukanyozela muzatenga matsoka
Osalora azako aziku locker
Kwanu Ndi Kwanu mmhu
Nthengo mudalaka njoka aah
Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Munachoka kunyumba kalekale mwati munatola Ka joker
Koma muzabwerabe kwanu nthеngo munalaka Ka njoka
Mwasintha mawanga mwasintha khungu mapeto Ake ndi matsoka
Muzatipeza zinthu zikazavuta Pano tingopеnya ndi maso
Pa maliro simumapezeka
Kumanda simumapezeka
Koma kuti mugone pansi lero lomwe kumanda omwewo mupezeka
Anapita kalekale kokawonekela eh
Koma kaphiri kakwawo sikaonekela eh
Pena nkumati njokayo mwina nthengo yasochela
Koma azatipezabe mizimu sikukondwera
Kwanu Ndi Kwanu mmhu
Nthengo mudalaka njoka aah
Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Yeah
Galu amanyada pakwawo nanga iweyo ulekelanji
Uzigomela Malawi kwanu kuno sungasowe mtaji
Funsa neba amasililanji
Mtendere umayambila chitipa kuthela Ku nsanje
Warm heart Ku mpanje
Uzingotakata mpakana uzatsegula maloko
Kutukula Dela lakwanu akhale ako maloto
Kwanu usakuluzile hope
Ukavaya abroad kusaka guap
Tsiku lomwe uzafike pa top
Kwanu uzakuyikeso pa map
Mukanabwera
Mwakhalitsa
Anzanu ochenjela
Goshen amangitsa
Lemme explain
Kulibeko Malo ngati pa den
Tufunika mindset change
Osangokhalila kupanga complain
Yeah yeah
Kwanu Ndi Kwanu mhuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mhuuu
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mhhu eh
Ndi kwanube
Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh
Ndi kwanube
Nthengo mudalaka njoka aaah
Kamdothi iwe bwerera Ku nyumba iwe
Kamdothi iwe uthela moyenda iwe
Kamdothi iwe aaaaaah
Kamdothi iwe aaaaaah
Kwanu Ndi Kwanu mfana
Town ikasolobana
Ukumbuke padzana
Bwerera Kwa Amama